![Wezi Wezi](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/11/27/41ee7dfffae64e55805780b920e22d8dH3000W3000_464_464.jpg)
Wezi Wezi Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2024
Lyrics
Wezi wezi ndikukwela
Ndine dolo ine sine nfana ogwela
Komwe nduchokela palibe ankandimvela
Pa top pompo ndipomwe ndikubwela
Mmmmh Wezi wezi ndikubwela
Ndine dolo ine sine nfana ogwela
Komwe nduchokela palibe ankandimvela
Pa top pompo ndipomwe ndikubwela
Ooh Wezi wezi ndikukwela
Pano ngini ingotheka
Pano ngini ingowekha
Pano ngini ikuphweka
Ooh Wezi wezi ndikukwela
Pano ngini ingotheka
Pano ngini ikutheka
Pano ngini ingoweka
Pano ngini ikuweka
Pano ngini ikuphweka
Eyy, we thank God
Ooh m
Wezi wezi ndikukwela
Ena kulakala kuphwekesa kwawo atapanga rewind
Ena amatembelera kulankhula ati mzungokhala behind
Wezi wezi ndikukwela, ndikuzakhala pa top
Move the masses I pop (Pope)
Ndine Mash sine flop
Ndine Mash sine flop
So, raise your hand ngati munandiphushako kuti ndiblowe
Raise your hand ngati munandithandiza kuti ndi growe
Ndinkadya ma frus, kukhuta, ndikumwela madzi
Kupempha fans mzindi supporter, tikule limodzi
Kuphusha left - right ine stereo
Ku switcher level ine stereo
Sungalimbane ndi believer
Mwatenthedwa ine fever
Kuphusha dream osatopa
Onsewa anayambila pompa
Ma fans anga akundiphusha osafooka
Ooh Wezi wezi ndikukwela
Pano ngini ingotheka
Pano ngini ingowekha
Pano ngini ikuphweka
Ooh Wezi wezi ndikukwela
Pano ngini ingotheka
Pano ngini ingoweka
Pano ngini ikuweka
Pano ngini ikuphweka
Eyy, we thank God
Ooh Wezi wezi ndikukwela
Ndine dolo ine sine nfana ogwela
Komwe nduchokela palibe ankandimvela
Pa top pompo ndipomwe ndikubwela
Mmmmh Wezi wezi ndikubwela
Ndine dolo ine sine nfana ogwela
Komwe nduchokela palibe ankandimvela
Pa top pompo ndipomwe ndikubwela
Ooh Wezi wezi ndikukwela
On ma way
Ndikukwela
On my way
Ndikukwela
On my way
Ndikukwela
Ndikukwe
On my way to the top
Ndikukwe
On my way to the top
Ndikukwe
On my way to the top
Ndikukwe
On my way
Ndikukwelaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaa.