![Akuzike ft. Beracah & Siggy Kim](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/06/26/fb407208c13d4579bc6a825a4b628a7a_464_464.jpg)
Akuzike ft. Beracah & Siggy Kim Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2023
Lyrics
Ey
Ambuye
Mwandichotsa kutali
Olo nditani matengabe yanga mbali
Sindingakutayeni ntakhala millionaire
Moyo ndi wanu mumatipatsa million air
Mpweya waulele
Moyo waulele
Munatumiza mwana wanu kuti azandifele
Alipo ena akuvutika muchipatala
Ndi chibwana chabe chosakonda church koma bara
Mwandikondera
Ndiye ndikuti zikomo
Ndikukondeni mu mtendere ndimuzikhomo
No lorry kodi yesuyo wantani?
Kuti akudalitseni motere man
Nthawi zambiri nkamawelenga madalitso is wealth
Ndimaiwala zinthu ngati good health
Ambuye akuzike
You make me win battles that I cannot see ngati ine Baba Vos
Mwayenera
Ulemu mwayenera
Pomwe ndimalephera
Tate mumandigwila dzanja
Mbuye wanga you give everything
More than I've ever needed
Muzonse ndidutsamo
Nyimbo yanga ndi
Akuzike akuzike
Akuzike akuzike
Akuzike akuzike Yahwe
Yeah
Atamandike atamandike
Akuzike akuzike
Akuzike akuzike Yahwe
Munandithyolera nde nde siza Paulo ndi Sirah basi
Mwana wa atate nde sindingasinthe syllabus
Ndisinthe ndilalike za mudziko?
Haaaa iweee!!
Moyo ndi wake nde ndimukwezeke Yahweh
Akuzike
Munadalitsa kupanga kuti malire akuzike
Mwandipatsa zofunika komanso chimoyo cha thanzi
Simphamvu zanga kupeza zonsezi
Opanda inu sindingayesele olo wezi
Mwandikweza kuchoka pa Mira pano pa Benz
Kundidziwa nsanabadwe and you know the number of my days
Athu ndi mapulani inu makhazikitsa
Muli nafe pulani inu simulakwitsa
Nzeru ndikulimbika inu munatipatsa
Mundikweze pomwe adani afuna kunditsitsa
Mwayenera
Ulemu mwayenera
Pomwe ndimalephera
Tate mumandigwila dzanja
ooh you give everything
More than I ever needed
Muzonse ndidutsamo
Nyimbo yanga ndi
Akuzike akuzike
Akuzike akuzike
Akuzike akuzike Yahwe
Yeah
Atamandike atamandike
Akuzike akuzike
Akuzike akuzike Yahwe