Kulimbika (Radio Edit) Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2024
Lyrics
Kulimbika tikulimbikila
Zivute Zokha
Kukankha nde Takankha
Si Lero Lokha
Kuyesa Kuphusha ngini osafooka
Step kuponya step tioloka
Tizapuma Kumwamba
Tizapuma Kumwamba
Tizapuma Kumwamba
Tizapuma Kumwamba
Kulimbikila Chonchi
Mpaka masten ayendele Benz
Kulimbikila Chonchi
Abale anga asamalipile rent
Tizapuma Kumwamba
Tizapuma Kumwamba
Tizapuma Kumwamba
Tizapuma Kumwamba
Kulimbika tikulimbikila
Zivute Zokha
Kukankha nde Takankha
Si Lero Lokha
Kuyesa Kuphusha ngini osafooka
Step kuponya step tioloka
Tizapuma Kumwamba
Tizapuma Kumwamba
Tizapuma Kumwamba
Tizapuma Kumwamba