Ndalama Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2023
Lyrics
Ndalama - Trappybeats.
...
Ndakuthela Ma Plan
Ndipange Bwanji
Kodi Nnalakwa Chani
Kuchulusa
Miseche Ndizi Nkhani
Chifukwa Cha!
Ndalama Ndalama
Maluzi Ndatchekela
Ulimi Nnayesa Kale
Ku runner ma taxi
Funa ma tip
Kusaka money tiguleko drip
Ndalama Ndalama Ndalama Ndalama Satana
Kudzuka mma three ku den pita mma ten
Osagona kusaka ma change
Kudzuka mma three ku den pita mma ten
Osagona kusaka ma change
Ndaleka ndaleka zibwanazo ndaleka
Ndatopa Ndatopa Eh Zandicheka cheka
Ndakuthela Ma Plan
Ndipange Bwanji
Kodi Nnalakwa Chani
Kuchulusa Kuchulusa!
Miseche Ndizi Nkhani
Chifukwa Cha! Chifukwa Cha!
Ndalama Ndalama
Nkhani ndikunvana
Nkumasaka Ndalama
Mpakana Kudana Kamba ka ndalama
Nkhani Ndikunvana
Nkumasaka Ndalama
Maluzi Maine
Wandisiya Mmalere
Usandiuze Maine
Ndingosaka Mandede
Ndalela Ndaleka
Maluzi Maluzi Maluzi
Maluzi Maluzi Maluzi
M'siye Nzako
Maluzi Maluzi Maluzi
Maluzi Maluzi Maluzi
M'siye Nzako
Ndakuthela Ma Plan
Ndipange Bwanji Ndipange Bwanji!
Kodi Nnalakwa Chani
Kuchulusa Kuchulusa!
Miseche Ndizi Nkhani
Chifukwa Cha! Chifukwa Cha!
Ndalama Ndalama