Weekend ft. Fada Moti Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2023
Lyrics
Eh!
Eh
Eh eh
Internationally ting say,
Eh eh
Tifela weekend (aah aye)
Tifela weekend (aah aye)
Tifela weekend (aah aye)
Tifela weekend (aah aye)
Motily Moti
Tifela Weekend musabalalike
Lerolo bayala alire
Asanafike adabwitsike payende mowa ngati mtsinje
Tifela Weekend musabalalike
Lerolo bayala alire
Asanafike adabwitsike payende mowa ngati mtsinje
Wabwera wekha ndabwera ndekha ndekha
Iwe tadekha umbombo taleka leka
Wabwera wekha ndabwera ndekha ndekha
Iwe tadekha umbombo taleka leka
Adekhe (Masese)
Adekhe (Masese)
Adekhe (Masese)
Adekhe (Masese)
Adekhe (Masese)
Tifela weekend (aah aye)
Tifela weekend (aah aye)
Tifela weekend (aah aye) (adekhe masese)
Dziko lonse kwakoma ndikuno
Dziko lonse pakoma ndipano
Fada wa Vunga Plan
Lero Tiichemesadi
Aliyense Azipanga zake
Maluziwo isandipake, Poti
Wabwera wekha ndabwera ndekha ndekha
Iwe tadekha umbombo taleka leka
Wabwera wekha ndabwera ndekha ndekha
Iwe tadekha umbombo taleka leka
Adekhe (Masese)
Adekhe (Masese)
Adekhe (Masese)
Adekhe (Masese)
Adekhe (Masese)
Tifela weekend (aah aye)
Tifela weekend (aah aye)
Tifela weekend (aah aye) (adekhe masese)