Kulera Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2024
Lyrics
Wazizur
My father
My father
My father
You my hero my father
Kushupha kwanu kunandisamala
Your discipline ndithu zina saver Mnyo wanga
Kupanda mambama aja bwezi pano nditafa
Ndi ushasha wa mu ghetto mu ghetto sitinkamva
My father
Experience yokhala ndi mwana
Munalibe munayambila pa ine ndi mama
Tailora my mama
Anthunu munkamvana
Imfa inachita njilu msanga
Bwezi pano tikuseka za mwana wa ine
bwezi pano tikupanga za ukwati wa ine
Bwezi pano tiku panga za
Kulera ineyo kulera
Kulera ineyo kulera
Kulera ineyo kulera
Kulera ineyo kulera
Kulera kulere kulera
I have seen you lose
I have seen you win
Ndakuonani mutapenga ndi ma fees
Ndakuonani mukuseka mutakwiya
Palibe tsiku lomwe munamenyapo mayi anga kick eishh
you not perfect dad
I'm thankful for your presence in our fragile lives
Munakatha kuthawa nkutisiya panja
mphepo nkutikantha mantha n'nalibe ndi inu father
Kulera ineyo kulera
Kulera ineyo kulera
Kulera ineyo kulera
Kulera ineyo kulera
Kulera kulere kulera
Kulera
Kulera kulera kulera
Kulera
Kulera kulera kulera