Ku Mpanje Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2024
Lyrics
Wazizur
Zochitika ku mpanje nje nje nje nje
Njala nthenda ndi nsanje nje nje nje nje
Kukhala ngati makape pe pe pe pe
Flames yakhala manje nje nje nje nje
Zochitika ku mpanje nje nje nje nje
Njala nthenda ndi nsanje nje nje nje nje
Kukhala ngati makape pe pe pe pe
Flames yakhala manje nje nje nje nje
Zochitika ku mpanje
I was on fb dzulo ku scroller
Ndapeza news mfana wa ku dowa
Mbuzi goat ya ku dowa
Yapanga magetsi man zinthu zosowa
Ena ati amunyongatu
Mfanayu ndi zoba atiwotcha
Ena ali busy kumupopa
Ziyende bwino amupase scholarship mu boma
Siziyenda choncho
It's frustrating ukakhala Mtondo
Tikamaiyanganila mmusi izingothawila kunja mitondoyi
Kulandila theche mmalo mwa nkono
Tigona bwanji mutapha maloto
System yosamva magobo
Titsegula bwanji dziko titabisa maloko
Ku Mpanje nje nje nje nje
Njala nthenda ndi nsanje nje nje nje nje
Kukhala ngati makape pe pe pe pe
Flames yakhala manje nje nje nje nje
Zochitika ku mpanje
Kuno ndi bola
Tizingovutika tonse bola
Wina akangoiphula ndi mbola
Iweyo ngati ndani uzi baller
Tili allergic to success
Nzanga akangoiphula ngati ndi sanze
Utha kudabwa ndizochitika pa mpanje
Tonse a ku bt koma busy ndi nsanje ehh olo mukatche
Komanso ukaiphula eti
Uzidziwa safunsa anadya phula eti
Ndi ma friends omwewa amakupasa pressure uziliva modula eti
Zinazi sitiuzana
A couple years later nzako uja wamanga
Chi den chake unali busy ndi kuyaka
Kenako mmazayambapotu kulozana
iwe anthu amaphana ku mpanje
Nje nje nje nje
Njala nthenda ndi nsanje nje nje nje nje
Kukhala ngati makape pe pe pe pe
Flames yakhala manje nje nje nje nje
Zochitika ku mpanje nje nje nje nje
Njala nthenda ndi nsanje nje nje nje nje
Kukhala ngati makape pe pe pe pe
Flames yakhala manje nje nje nje nje
Zochitika ku mpanje