![Yekha ft. Aidfest Madness](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/04/06/d9f5098353ca40e58cccd4d94db1293b_464_464.jpg)
Yekha ft. Aidfest Madness Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2024
Lyrics
Yekha ft. Aidfest Madness - Kineo Madness
...
Kaya mukuti mamuna ndi wagulu alindi ankaz chimulu koma aka mabwera kwathu a(mabwera yekha)kaya mukuti nkaz ndi wagulu ali ndi amuna chimulu koma aka mabwera kwathu a(mabwera yekha) yekha yekha yekha yekha (a mabwera yekh) yekha yekha yekha yekha(amabwera yekh)
Uyu ndiwang wang bas ndasaina (ndasainabas)kaya mukut mamuona kut ndi wina koma akabwera ndiwang bs athu akaduka inu chaka chino muva(nbenbe)akapasule ine chaka chino muva (nbenbe)athu akaduka chaka chino muva (nbenbe) akapasule inu chaka chino muva (bebe)
Kaya mukuti mamuna ndi wagulu Ali ndi ankaz chimulu koma akamabwera kwathu (amabwera yekha) kay mukuti nkaz ndi wagulu ali ndi amuna chimulu koma akamabwera kwathu (amabwera yekh)yekh yekha amabwera yekh
All no no no (oh no) musandiuze kut nditaye uyuyu(aaah)taona mene akuonekela bwino ndinasakha kale kaleuyuyu akakakokha kwa ine ndimakina ndatola joker mutisiye muchedwa akakakokha kwa ine ndimakina ndatola joker mutisiye michedwa
Kaya mukuti mamuna ndi wagulu Ali ndi ankaz chimulu koma akamabwera kwathu (amabwera yekha) kay mukuti nkaz ndi wagulu ali ndi amuna chimulu koma akamabwera kwathu (amabwera yekh)yekh yekha amabwera yekh