Anzanu ft. Aidfest Madness, Zeze Kingston, Leumas & Richard Billy Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2023
Lyrics
Zeze Kingston
]
Ayo! Billy
Hmhihihi Serato
Aye
Aye
Aye
Aye
(Ayo Tiyeni!)
Aye ay
Ayy ay
(Tiyeni! Tiyeni! Tiyeni!)
Ay ay (Eish!)
Koma awa kulongolola
Koma awa kulongolola
Matukutuku adzawapweteka (Pweteka)
Matukutuku adzawapweteka (Mmh)
Koma awa kulongolola
Koma awa kulongolola (Iyee Iye)
Matukutuku adzawapweteka (Ayiyaya ya)
Matukutuku adzawapweteka (Ayiyaya ya)
Umangolonjeza
Koma kanthu suchita
Koma inu kunamiza
Kutipusitsa
Umangolonjeza,Koma kanthu suchita (Iyee Iye)
Iwe Koma kunamiza
Kumangotipusitsa
Umangotilonjeza (Iyee), Umangotipusitsa (Iyee)
Umangotinamiza (Iyee), Umangotinamiza (Iyee)
Umangotilonjeza (Iyee), Umangotipusitsa (Iyee)
Umangotinamiza (Iyee), Umangotinamiza (Iyee)
Washii!
Anzanu Anzanu amangochita Anzanu
Salubwalubwa Anzanu, Amangochita Anzanu
Anzanu Anzanu amangochita Anzanu
Salubwalubwa Anzanu, Amangochita Anzanu
Anzanu Anzanu amangochita Anzanu
Salubwalubwa Anzanu, Amangochita Anzanu
Anzanu Anzanu (Ay!) amangochita Anzanu (Ay!)
Salubwalubwa Anzanu (Ay!),Amangochita Anzanu. (Ay!)
Iyee
Iye iyee
Iyee
Iye iyee
Iyee (Ayo Tiyeni!)
Iye iyee
Iyee (Tiyeni! Tiyeni! Tiyeni! eish!)
Iye iyee
Mwanena ichi, Mwanena ichi
Ife timangongo kumverani
Koma mumangolubwa sumumachita
Mwati mukupusitsa ndani?
Mwanena ichi, Mwanena ichi
Ifе timangongo kumverani
Koma mumangolubwa sumumachita
Mwati mukupusitsa ndani?
Koma mumati Abwanawo Kuno ndi Azoba Iwo
Khalidwe lawo ndilopusa iwo
Abwanawo Kuno ndi Azoba Iwo
Khalidwe lawo ndilopusa iwo
Amangotilonjеza, Amangotipusitsa
Amangotinamiza,Amangotinamiza
Umangotilonjeza,Umangotipusitsa
Umangotinamiza, Umangotinamiza
Washii!
Anzanu Anzanu amangochita Anzanu
Salubwalubwa Anzanu, Amangochita Anzanu
Anzanu Anzanu amangochita Anzanu
Salubwalubwa Anzanu
Amangochita Anzanu
Anzanu Anzanu amangochita Anzanu
Salubwalubwa Anzanu, Amangochita Anzanu
Anzanu Anzanu (Ay!) amangochita Anzanu (Ay!)
Salubwalubwa Anzanu (Ay!), Amangochita Anzanu (Ay!)
Washiii
Umangolonjeza
Koma kanthu suchita
Koma kanthu suchita
Koma kanthu suchita
Umangolonjeza
Koma kanthu suchita
Koma kanthu suchita
Koma kanthu suchita
Umangolonjeza
Koma kanthu suchita
Koma kanthu suchita
Koma kanthu suchita
Umangolonjeza
Koma kanthu suchita
Koma kanthu suchita
Koma kanthu suchita
Umangolonjeza
Koma kanthu suchita,Koma kanthu suchita,Koma kanthu suchita
Washiii!
Ish!, Ish!, Eh!
Ish!, Ish!
Ih!,Ih!,Ih!, Ih!
Washiii!
Washiii!