![TWO TWO](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/05/25/2c68c998a6974a9094a12939962a9433_464_464.jpg)
TWO TWO Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2023
Lyrics
TWO TWO - Kineo Madness
...
Pa chigibo Pearson izithela ma penalty
Kukongola kwake ukuku iwe
Ndili nawe jealousy
Ukumandidusadusa apa ndingo feeler
Pain ase
Nkundisiya ine kukasakha uyo
Umaganiza chan ase
Dikila ndiwine premier bet
Ndalamayo ndi kugulire chi Benz
Or ufuna guccie or fend
Tangondisakha ndi wine kampen
Dikila ndi wine bet
Ndalama yo ndikugulire chi Benz
Or ufuna Gucci or fend
Tandondsakha ndi wine kampen
CHORUS
Two two kalipo lipo ×5