![Anawa](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/03/08/16690fc6052f48c389a07e9c0b818a55_464_464.jpg)
Anawa Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2024
Lyrics
Anawa - Big C Uncle Big
...
Aaaaaa
Big C
Uncle
Biggie
Intro :
Sikuti analakwitsa kukhala nazo ndalama , makolo awo
Ndikuti sanalakwe kuwapansa zofunikira mmoyo wao anaaaawa
Anawa bambo awo anali Pwepwete,
Anzathu sanamveke akulira lawo linali phwete.
Zowawa ankalavula anali phwetekere,
Nanga alira chani alekeni ana asangalale.
Nthawiyo tikulira nayo life Chitakhumbila anzathu akuphaka yawo life.
Tsono big mistake anachita ndikutukwana, kudelera onse akuchepekedwa.
It came to worse anamela mapiko mpaka kutukwana mlengi yemwe anawalenga.
Palibe chikuyenda,
Ati ali ndi tsoka,
Ati anawalodza, chibwana
Anakula moyo opusa anawa,
Kudzitenga ngati achuma anawa
Bambo wawo anawasiya anawa
Ndakapolo angovutika anawa
Mukamawanyengelera anawa
Mudziwe mkuononga anawa
Tsiku lina mdzawasiya anawa
Dziwani adzavutika anawa
Anakula moyo ophweka anawa
Anakula odelera anawa
Anakula mopepela anawa
Ndi chifukwa angovutika anawa
Akaphwanya Malamulo ankafunika chilango anzathuwa sanalangidweko,
Zoti moyo siuli simple tsiku lina akafikapo izi sanaudzidweko.
Ku school ankajomba they didn't go, yeah anasiya ku mbuyo goal.
Akaona olumala ana azimva Chisoni, my granny taught this long ago.
Kukacha mwanozolowela kukhala phwi, akakula kutsogolo Mavuto pa Iye ali phwi.
Adzakhala mmaluzi, didn't follow the rules ,kuchita kusowa lamba kumangila luzi.
Anakula moyo opusa anawa,
Kudzitenga ngati achuma anawa
Bambo wawo anawasiya anawa
Ndakapolo angovutika anawa
Mukamawanyengelera anawa
Mudziwe mkuononga anawa
Tsiku lina mdzawasiya anawa
Dziwani adzavutika anawa
Anakula moyo ophweka anawa
Anakula odelera anawa
Anakula mopepela anawa
Ndi chifukwa angovutika anawa
Nthawi yoti Mwina akanapanga zawo,
Iwo busy kudzitukumula ndi Chuma cha bambo awo
Eya phunzilani through a mistake,
Dziko liphunzitsa lokha pano likuti Mavuto awo
Munachitilanji, kudzitenga boss ntchito msanagwire,
Nthawi yafikapo ndati wow
Munkaganizanji, nokha kudzitchula opambana,
Anzanu osationa pano ndati bow
Zikupweteka ku mtima ndikukamba I know
Chilungamo sichikuopa chipambano
Ndipo zoti kugwira ntchito mukuopa I know
Respect tomorrow because you never know
Anakula moyo opusa anawa,
Kudzitenga ngati achuma anawa
Bambo wawo anawasiya anawa
Ndakapolo angovutika anawa
Mukamawanyengelera anawa
Mudziwe mkuononga anawa
Tsiku lina mdzawasiya anawa
Dziwani adzavutika anawa
Anakula moyo ophweka anawa
Anakula odelera anawa
Anakula mopepela anawa
Ndi chifukwa angovutika anawa
Akufuna pamalo panga pakhale Pake no no
Anamela nsanje yaikulu yopanda Pake uyo uyo
Chidzaimba ng'oma cha misala tsiku lija ndi lero, lero
Mpaka kumvalira nyau zithera nkuvina hello, No No