![Nambewe](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/02/19/56fd2c25509d4785b49d8e7ac7f14263_464_464.jpg)
Nambewe Lyrics
- Genre:Afrobeat
- Year of Release:2024
Lyrics
Nambewe - Big C Uncle Big
...
Aaaaaa
Big C
Uncle
Biggie.
Ngati ena ankalengedwela mchenga, iwe ndi mwala //
Anayamba kulenga ena chautayo, iwe ndi wotsilizira //
Mmaso mwanga siuchoka, chikhale nditagona ndimakuonabe //
Mtima wanga waupwetekapweteka kulibe ofana nawe,,
Enawa ndi kuchigwa, pa iwe ndinafika pa mtunda //
Kupanda kukuona ndimayamba kubanika mtima umagunda //
Sin'khulupilirabe makamaka ukandiuza umandikonda //
Sindidzitengela macheza nde ndikutengela kwa makolo wanga //
Makolo anga akhale ako //!!
Pano nde pakwathu wafika masuka,
Icho ufuna kuchita Chita Chita,
Icho ufuna kutenga tenga tenga,
Pano nde pakwathu wafika masuka,
Nambewe, Nambewe
Nambewe, Nambewe //!!!!
Sono mvera Nambewe,,
Sindinati, pamudzi pano ukhale mfumu //
Sindinati, bambo wanga udziwadelera //
Sindinati, mayi anga ndi saizi yako //
Sindinati, abale anga udziwamenya //
Mukazi wa nzeru, amadziwika ndi khalidwe //
Akakhala opusa amaononga banja ndi manja ake //
Chonde Nambewe, ndisungile mau yawa //
Kuli anthu otiona, asadzatiseke pamawa //
Ngati ena ankalengedwela mchenga, iwe ndi mwala //
Anayamba kulenga ena chautayo, iwe ndi wotsilizira //
Pano nde pakwathu wafika masuka,
Icho ufuna kuchita Chita Chita,
Icho ufuna kutenga tenga tenga,
Pano nde pakwathu wafika masuka,
Nambewe, Nambewe
Nambewe, Nambewe //!!!!
Tikaone asibweni ku Mzimba,,
Uyu ndiye Nyambewe mwana wakwa Mbewe, ku Lilongwe //
Wakukana masebela kumuyamba dala mulirenge //
Ndipo nkhalo yakudelera wakamwana chaka Chino muileke //
Imwe mukutimbanizga nthengwa zabanyinu, vilekeke //
Nthengwa mbanthu babili ine na Nyambewe, tikhalenge //
Enya tilije napakwambila kwe chiuta watumbikenge //
Musatitenge ma advantage inu achina Maiko //
Biliwita yemweyu ndidzapita naye akunja Maiko //
Ngati Sarah wa Abraham adzakhala mayi Maiko //
Ndani sanaone mkazi wa mphamvu kuno wamphamvu aliko //
Pano nde pakwathu wafika masuka,
Icho ufuna kuchita Chita Chita,
Icho ufuna kutenga tenga tenga,
Pano nde pakwathu wafika masuka,
Nambewe, Nambewe
Nambewe, Nambewe //!!!!.
Pano nde pakwathu wafika masuka,
Icho ufuna kuchita Chita Chita,
Icho ufuna kutenga tenga tenga,
Pano nde pakwathu wafika masuka,
Nambewe, Nambewe
Nambewe, Nambewe //!!!!