![Enemies of Progress](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/03/24/bff7705d81ac486bb8a6602c38a46850_464_464.jpg)
Enemies of Progress Lyrics
- Genre:Afrobeat
- Year of Release:2024
Lyrics
Enemies of Progress - Big C Uncle Big
...
Osayang'na kumbaaali, let's have eye contact //
Zomwe ndifuna kukamba, sindinalipidwe contract //
Mwati bola akutali, ine m'bale wanu, mulibe yanga contact //
Ndinafa kale mmaganizo mwanu kuli bwanji body contact //
Mzanga kuchita bwino kwako, ambiri mwa iwo chiwawawa //
Zindikira amangoseka nawe mkati mwao mitima imatupa //
Let me shock you, mmunda mwako muja akudzalira nansongole //
Let me tell you alibe ndi chifukwa China afuna usadzakolore //
Pakuti we grow by lifting others nginde inawapitilira //
Zoti timakuuula potukula ena anthu Ena sadzidziwa,
Ndiwo amatchedwa//
*Hook*
Enemies of progress
Chimwemwe chawo in your tears
Enemies of progress
Amakondwa when you gain less
Enemies of progress
Samalimbika ndi aulesi
Enemies of progress
Zikakuvuta amati yes
Enemies of progreeeess
Chimwemwe chawo in your teaaaaaars
*Verse 2*
Ndisatsogolere,
Akufuna nditsalire ine Eeeee //
Dzuwa silingalowe,
Asanandinamizile ine Eeeee //
Adzimitsa nyale,
Yoti yindiwunikile Eeeee //
Mbuye mkhale nane,
Ndiopa angandipweteke Eeeee //
Chabwino choti chifuna ine,
Apeleka kwa anzanga ine Eeeee //
Ambuye mukundimva,
Mundionetsele zanga ine Eeeee //
Awa ndi a boss,
Koma ndi ansanjenso //
Kakuchepako mpakaanyemekonso //
Pakuti we grow by lifting others nginde anawapitilira //
Zoti timakuula potukula ena anthu ena sadzidziwa //
Ndiwo amatchedwa.
*Verse 3*
Nthawi ikakwana,
Tiivomelezeeee //
Mzathu akakondwa,
Timsangalalireeee //
Mijedu, nsanje,
Sidzingatipindulireeee //
Namalenga ndiye,
Atisamalireeeee Ee Ee Ee.
Dziko ndilodzungulira ngati dzira,
Kwithu ku mzimba, chikuzweta nga nibola //
Munawina dzulo, ine ndawina lero sibweni vinthu nintheula vili nga nibola //
Pretend ngati zoipa zawo siwuona,
Litutuzgile kunthazi bola! //
Ovutika ndiwo poti matenda anatenga ndiwo,
Kumbukira, sanje ikujumpha ebola //
Tikule potukula ena zikhoza kutithandiza,
Zoti timakuula,
Potukula ena,
Anthu Ena sadzidziwa,
Ndiwo amatchedwa //