![Thandizo](https://source.boomplaymusic.com/group2/M00/4F/7E/rBEeNFnkdWKAbikhAAC6sz6wXGo776.jpg)
Thandizo Lyrics
- Genre:Afrobeats
- Year of Release:2017
Lyrics
Thandizo - Fishers Of Men
...
mumoyo wanga ndimalaka laka kunkala wokondwa mumoyo wanga ndima funa funa kunkala osekela ine koma zonse ine ndalepela kuzikwanisa cifukwa chace ine ningo pempa thandizo kwa inu. (×2)