![Chipulumutso](https://source.boomplaymusic.com/group1/M00/4F/D6/rBEeMVnkdbGAJO6rAADZZ-FhNYM465.jpg)
Chipulumutso Lyrics
- Genre:Afrobeats
- Year of Release:2017
Lyrics
Chipulumutso - Fishers Of Men
...
yeah yeah eh eh
yeah yeah eh eh
ahhh ahhh ahhh ahhh
cipulumuso chamoyo wanga
ndicho chikondwelelo cosatha
cipulumuso chamoyo wanga
ndicho chikondwelelo cosatha
anavekedwa korona waminga kupulumusa ine ocimwa.
navekedwa korona waminga kupulumusa ine ocimwa.
ahhh ahhh ahhh ahhh ahhh ahhh
nthano yacisoni(talala tala)
anasenza mtanda( mbuye ehheeh)
kuti one ndi pulumuke
nthano yacisoni anasenza mtanda oh kuti one ndi pulumuke
anavekedwa korona waminga kupulumusa ine ocimwa
anavekedwa korona waminga kupulumusa ine ocimwa
ahhhh ahhh ahhh ahhh
ahhh ahhh ahhh
cipulumuso chamoyo wanga
ndiyamika Inu ambuye
cipulumuso chamoyo wanga ndicho chikondwelelo cosatha
.................