![Ndapeza Mwai](https://source.boomplaymusic.com/group1/M00/4F/D6/rBEeMVnkdbGAJO6rAADZZ-FhNYM465.jpg)
Ndapeza Mwai Lyrics
- Genre:Afrobeats
- Year of Release:2017
Lyrics
Ndapeza Mwai - Fishers Of Men
...
ndapeza mwai kutimikira
ambuye wanga wachikondi
sindizaleka kutumikila
rmpaka tu imfa mbuye wanga
sindizaleka sindizaleka kumuimbila mbuye wanga
anandifela pamtanda paja
ndizayamika nthawi zonse
Ena akana kutumikira
ati ndacepa sininga kwanise
koma ineyo ndinalonjeza
kutumikila nthawi zonse
sindizaleka sindizaleka kumuimbila mbuye wanga anandifera pamtanda paja ndizayamika nthawi zonse
sindizaleka sindizaleka kumuimbira mbuye wanga anandifela pamtanda paja ndizayamika nthawi zonse..............