
Fanizo La Tiligu
- Genre:Others
- Year of Release:2024
Lyrics
Mmmmmmh ooooooh ooooooh Akuzike Thawe yeahhhhhhhhh eeh eeh
Ufumu wa Kumwamba ufanizidwa ndi munthu, amene anafesa mbeu zabwino m'munda mwake; koma m'mene anthu analinkugona, mdani wake anadza, nafesa namsongole pakati pa tiligu, nachokapo
Koma pamene mmera unakula, nubala chipatso, pomwepo anaonekeranso namsongole
Kazilekeni zonse ziwili, zikulile pamodzi kufikira pakututa; ndimo m'nyengo yakututa ndidzauza akututawo, Muyambe kusonkhanitsa namsongole, mummange uyu mitolo kukamtentha, koma musonkhanitse tiligu m'nkhokwe yanga
Ndipo anyamata ake a mwini nyumbayo anadza, nati kwa iye, Mbuye, kodi simunafese mbeu zabwino m'munda mwanu? Nanga wachokela kuti namsongoleyo?
Koma pamene mmera unakula, nubala chipatso, pomwepo anaonekeranso namsongole
see lyrics >>
Similar Songs
More from Akuzike Thawe
Listen to Akuzike Thawe Fanizo La Tiligu MP3 song. Fanizo La Tiligu song from album Acts Of The Apostle is released in 2024. The duration of song is 00:03:37. The song is sung by Akuzike Thawe.
Related Tags: Fanizo La Tiligu, Fanizo La Tiligu song, Fanizo La Tiligu MP3 song, Fanizo La Tiligu MP3, download Fanizo La Tiligu song, Fanizo La Tiligu song, Acts Of The Apostle Fanizo La Tiligu song, Fanizo La Tiligu song by Akuzike Thawe, Fanizo La Tiligu song download, download Fanizo La Tiligu MP3 song