Chifukwa
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2024
Lyrics
Moyo umatibwetsela zambiri
Zina zotiwawa
zina za Chisoni kwambili
Sizimatengela pomwe ife tili
Kapena kuti ndikoyamba kaya kachiwili
Koma Yesu atikondabe kwambili
Amakhala kuti watitchinjizira ku zambili
Kumbukila mawu ake akuti
Chikhulipililo chimasuntha mapili
Mu chikondi chake mantha alibe malo
Ndikudziwa ukumva ngati uli pa chibalo
kude bwanji dzula libwera mmalo
see lyrics >>Similar Songs
More from Faith DJ
Listen to Faith DJ Chifukwa MP3 song. Chifukwa song from album Chifukwa is released in 2024. The duration of song is 00:03:52. The song is sung by Faith DJ.
Related Tags: Chifukwa, Chifukwa song, Chifukwa MP3 song, Chifukwa MP3, download Chifukwa song, Chifukwa song, Chifukwa Chifukwa song, Chifukwa song by Faith DJ, Chifukwa song download, download Chifukwa MP3 song