Loading...

Download
  • Genre:Hip Hop & Rap
  • Year of Release:2024

Lyrics

Moyo umatibwetsela zambiri

Zina zotiwawa

zina za Chisoni kwambili

Sizimatengela pomwe ife tili

Kapena kuti ndikoyamba kaya kachiwili

Koma Yesu atikondabe kwambili

Amakhala kuti watitchinjizira ku zambili

Kumbukila mawu ake akuti

Chikhulipililo chimasuntha mapili

Mu chikondi chake mantha alibe malo

Ndikudziwa ukumva ngati uli pa chibalo

kude bwanji dzula libwera mmalo

Usiku uli ndi malile, satana alibe malo

Mu chikondi chake mantha alibe malo

Ndikudziwa ukumva ngati uli pa chibalo

kude bwanji dzula libwera mmalo

Usiku uli ndi malile, satana alibe malo


Tonthola usalile chifukwa

Kwa Iye ndiwe chifukwa

Usataye mtima chifukwa

Moyo wako uli ndi chifukwa

Nditonthola ine Chifukwa

Kwa Iye ndine chifukwa

Sinditaya mtima chifukwa

Moyo wanga uli ndi chifukwa


Nthawi zina sitimamvetsa

Ambuye ndi chani chikuchitika

Zimangokhala ngati alipo

Akufuna titafinyika

Koma kumbukilani mawu anena

Mdani wanthu si munthu ogwilika

Moyowutu ndi muuzimu

Ndipo padziko pano sindifetu mzika

Pukuta misonzi leza mtima

Chonde usataye mtima

Khulupila ndikuchita mawu Ake

Siumila, suwotcheka, moyo wako ndi wake

Pukuta misonzi leza mtima

Chonde usataye mtima

Khulupila ndikuchita mawu Ake

Siumila, suwotcheka, moyo wako ndi wake


Tonthola usalile chifukwa

Kwa Iye ndiwe chifukwa

Usataye mtima chifukwa

Moyo wako uli ndi chifukwa

Nditonthola ine Chifukwa

Kwa Iye ndine chifukwa

Sinditaya mtima chifukwa

Moyo wanga uli ndi chifukwa


Tipilize kupemphela

Tipitilize kudekha yep

Tipilize kuchenjela

Tipitilize kukhulupilila

Imva izi

Nyimbo y'a chiyembekezo

Imva izi

Nyimbo y'a chitinthozo

Imva izi mawuwa ndichenjezo

Maganizo oyipawo

Usamve zimenezo

Chita mbali yako

Mulunguso achita mbali Yake

Yesi anabwela ndi mpulumutsi wako

Ndiwe opambana maso Ake

Chita mbali yako

Mulunguso achita mbali Yake

Yesi anabwela ndi mpulumutsi wako

Ndiwe opambana maso Ake


Tonthola usalile chifukwa

Kwa Iye ndiwe chifukwa

Usataye mtima chifukwa

Moyo wako uli ndi chifukwa

Nditonthola ine Chifukwa

Kwa Iye ndine chifukwa

Sinditaya mtima chifukwa

Moyo wanga uli ndi chifukwa


Tonthola usalile chifukwa

Kwa Iye ndiwe chifukwa

Usataye mtima chifukwa

Moyo wako uli ndi chifukwa

Nditonthola ine Chifukwa

Kwa Iye ndine chifukwa

Sinditaya mtima chifukwa

Moyo wanga uli ndi chifukwa

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234
          -You can log in via below methods-
          Reset password via e-mail
          -or-
          Reset password via e-mail
          Feedback on resetting password
          * It may take a longer time

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status