
Ndiwebe
- Genre:New Age
- Year of Release:2019
This song is not currently available in your region.
Lyrics
Ndiwebe - Kell Kay
...
you already know yeah
sauko Peter sauko Peter this is for you
ndiwebe ndiwe wachikondi wangabe ndiweyo
bwanji tipitilize ife kukondanabe ife eh eh ifee
ndati ndiwebe ndiweyooo wachikondi wangabe ndiwey bwanji tipitilize ife kukondanabe ifee eh eh ifee
it's to you you are the one to be texting whole day long yeah you're the one to be calling whole night long yeah it's to you it's to you yeah
ndiweyo, yemwe tinkakhala osayambana kwa week yonse yemwe unkakhala osayang'ana zofooka zanga wawawa ndiweyo oh ndiweyoo (mpaka pano) timatha mwezi ife osayambana ife osanyozana ifee my baby ndipo ndizotheka kupitiliza apapa ifeee
ndiwebe ndiwe wachikondi wangabe ndiweyo bwanji tipitilize ife kukondanabe ife eh eh ife ndati ndiwebe ndiwe wachikondi wangabe ndiweyo bwanji tipitilize ife kukondanabe ife eh eh ife yoo
it's to you yemwe umandimvesa ine kukoma olo ukandisina yemwe simadanda olo kukwiya olo ukandiluma wawawa it's to you yeah it's to youu (ndiweyo) yemwe ukaphika umagwada pansi mbuye akudalise yemwe ukamachoka ndimamva kuwawa ukati ubayibise mamama ndiweyo ndiweyoo timatha mwezi ife osayambana ife osanyozana ife my baby ndipo ndizotheka kupitiliza apapa ifee
Lyric by Fra Kay
Similar Songs
More from Kell Kay
Listen to Kell Kay Ndiwebe MP3 song. Ndiwebe song from album Love After 24 is released in 2019. The duration of song is 00:03:28. The song is sung by Kell Kay.
Related Tags: Ndiwebe, Ndiwebe song, Ndiwebe MP3 song, Ndiwebe MP3, download Ndiwebe song, Ndiwebe song, Love After 24 Ndiwebe song, Ndiwebe song by Kell Kay, Ndiwebe song download, download Ndiwebe MP3 song
Comments (2)
New Comments(2)
wyson w
Chloe Thomson
[0x1f618]
man mumatha mumandisangalasa