Kuli dziko labwino
- Genre:Gospel
- Year of Release:2022
Lyrics
Kuli dziko labwino - Thoko Suya
...
Kuli dziko labwino m'Mwamba Lakuwala koposa dzuwa;
Yesu atikonzera malo
Pokhalira ife komweko.
Bwinoli tipita,
Tikumana mwa Dziko lija, Bwinoli tipita,
Tikumana mwa Dziko lija.
2 Tidzimba komweko nyimbo Za abwino omvera Yesu, Sitidzamva chisoni ife, Tidzakondwa masiku onse.
3 Tidzatama Atate wathu
Kuti Iye 'napatsa Yesu Kuchotsera zochimwa zonse, Ndi kutidalitsira ife.
Similar Songs
More from Thoko Suya
Listen to Thoko Suya Kuli dziko labwino MP3 song. Kuli dziko labwino song from album Hymns, Vol. 2 is released in 2022. The duration of song is 00:06:06. The song is sung by Thoko Suya.
Related Tags: Kuli dziko labwino, Kuli dziko labwino song, Kuli dziko labwino MP3 song, Kuli dziko labwino MP3, download Kuli dziko labwino song, Kuli dziko labwino song, Hymns, Vol. 2 Kuli dziko labwino song, Kuli dziko labwino song by Thoko Suya, Kuli dziko labwino song download, download Kuli dziko labwino MP3 song