
Ndi Hallelluya
- Genre:Gospel
- Year of Release:2022
Lyrics
Ndi Hallelluya - Thoko Suya
...
Ndi Aleluya imbirani
'Tate wathu, wakumwamba, Analenga zonse.
Chifundo chake chachikulu, Nzeru, mphamvu ndi ufumu Tiyamike tonse.
2 Ndi Aleluya imbirani
Yesu Khristu Mpulumutsi, Anachoka kwawo,
Nakhala munthu, pansi pano, Nasauka, natifera,
MULUNGU MMODZI MWA ATATU
4
Natisiyira mawu.
3 Ndi Aleluya imbirani Mzimu wake Wakuyera, Amakhala nafe. Atilangiza za Mulungu, Nayeretsanso mitima Ya akhristu ife.
see lyrics >>Similar Songs
More from Thoko Suya
Listen to Thoko Suya Ndi Hallelluya MP3 song. Ndi Hallelluya song from album Hymns, Vol. 2 is released in 2022. The duration of song is 00:07:57. The song is sung by Thoko Suya.
Related Tags: Ndi Hallelluya, Ndi Hallelluya song, Ndi Hallelluya MP3 song, Ndi Hallelluya MP3, download Ndi Hallelluya song, Ndi Hallelluya song, Hymns, Vol. 2 Ndi Hallelluya song, Ndi Hallelluya song by Thoko Suya, Ndi Hallelluya song download, download Ndi Hallelluya MP3 song