Dear Mahopu Five Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2021
Lyrics
Dear Mahopu Five - EvanzMuzik
...
Ndizobhowa kuti ndizingo kulembela makalata
Zawulemu basi zatha pano ndizingo lalata
Mesa nkhani idatha kalekale chaka chatha
Ine nkumati ndagwila muntima munali bata
Koma aa man koma aa ndaoneka kape
Iweyo wakhala star
olo kuyithoka fanzi pano imangoti sha
Zamanyazi dear mahopu andilanda adah
Ndipo........ Sazakuone mu hudu
Zakunkhwisila agalu ndizakuthila gututu
Kuku khwekhweleza pasi kukuchotsa wivi m'mutu
Ndiwe zoba muthokeso nzakoyo ndi bulutu
Udango kongola m'mtima wako ndiwa fisi
Uchoka bwanji chibwezi chilipo chachi wisi
Eti olo kiss eti olo aaaaa eti eti mahopu ine ndizakuthila chi fits
Mwina chifukwa ndimakonda kusunga tsitsi
Mwina kapena ndimaoneka wachimidzi
Kapena utchisi
Usazadabwe ukadzaona dzina lakolo lapezeka pa list
Coz nawe umva pain ndithu by any mean's
Nkazi otengeka ntimuloving things
Ku kukonda kokha saname ndidayetsetsa
Chifukwa chaiwe maluzi ankandi nyetsa
Ndaku tchesa zaka zambili mpaka kugwila
One week leter ena adzandi landila
Koma aaa man koma aaa
Chondiwawa nchoti mpaka ndinasiya bawa
Ndidasiya ganja osaphonya shower
Ndimayinitsi angati amene wandi kawa
Ine kuden kulengeza kuti ndapeza honey
Kukupanga introduce kwama sistezi aine
Kwama homez aine ma classmate aine
Ndani sadakuwone pamadipi aine
Palibe tsiku lomwe ndidakupephako ma nudes
Zoti pali wina mahopu sunandiuze
Ona ndayalukapo ndikhan zachabe chabe
Nzomvetsa chisoni kut ndimaku hopelabe
Ndimaku lotabe
Nzawusilu kuvomeleza ndika khalakhala ndimaku stokabe
Nkhope yako mutu mwangamu sikuchokabe
After khanza wandichita sindiku topabe
Udzaziwa day one kuti sine wafegi
Dolo wakoyo adzakaku patsa heart break
Muntima ukudziwa wapanga zosayenela
Iweyo jaja akuwone mapa deladela
Tikadza kumana pamalo padzatelela
Timatama tako toseto tidzakuthela
Olo usayakhe kalatayi palibe chovuta
Olo uwelengetse magaye
Koma mawu omaliza udzandifuna Iswear
Ndatha ine ex wako yemwe una player