
MABODZA Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2021
Lyrics
ase Tràpêr
ankati ineyo ndi mfana
mabodza
Chaka chino nde ndi changa ine
mumanama
ankati ineyo ndi mfana
mabodza
Chaka chino nde ndi changa ine
mumanama
ndina blower ndiku Banda
koma ndimadana ndizachamba
si ine mfana wa mu mpanda
but I gat skills in abundance
mwina ndizomwe ndimamangazi
kapena m'phasha ndimavalazi
Kwa ine akazi ndima dalazi
Kwa in akazi ndimadalazi
yeah
kumenya ma hit back to back track on track
rapper kubwela kupanga attack attack
koma osayankha ine si size yake
pitani mukauzane simungamake
ankati ineyo ndi mfana
mabodza
Chaka chino nde ndi changa ine
mumanama
ankati ineyo ndi mfana
mabodza
Chaka chino nde ndi changa ine
mumanama
see the dj play my sing at the bar
am a starrrrr, understaaaand