Kwanu Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2024
Lyrics
Chariz
Yeah
You my destiny
Don't worry about the girls
The other girls
Girl they're dead to me
Ndikupanga za Iwe, uli ndi ine
Come and dance with me (wind your waist Mamie)
I know you like my game I got game like a full pitch
Bwela pafupi, let's make a movie (50 shades)
Iwe ndi ine, we can do this
Zaifela ndizabwela ndi ankolo kwanu
Nzaikwela yazalewa kukulondola kwanu
Kuzalowola (kwanu)
Ku pheya lobola (kwanu)
Kapena ng'ombe mu khola (kwanu)
Tangondilola
Zaifela ndizabwela ndi ankolo kwanu
Nzaikwela yazalewa kukulondola kwanu
Sizakudyetsa thelele pa 1 mpaka pa 30
kukhala nawo Monday to Sunday
Singalole wina andilande
Bwela uyese uone ndikukhape
Uzakhala pakhomo pa mwana alilenji
Weekend Ku spender ku lake
Nzakusamala sizakupanga nkhanza
Zakukwela Ndiwe wako wako Tarzan
Zaifela ndizabwela ndi ankolo kwanu
Nzaikwela yazalewa kukulondola kwanu
Kuzalowola (kwanu)
Ku pheya lobola (kwanu)
Kapena ng'ombe mu khola (kwanu)
Tangondilola
Zaifela ndizabwela ndi ankolo kwanu
Nzaikwela yazalewa kukulondola kwanu
Kuzalowola (kwanu)
Ku pheya lobola (kwanu)
Kapena ng'ombe mu khola (kwanu)
Tangondilola
Kwanu kwanu yeah
Kwanu kwanu yeah