
Tsiku Lonse Lyrics
- Genre:Gospel
- Year of Release:2024
Lyrics
Ladies and Gentlemen
There's time for everything
It's time to praise Him
Oh oh oh oh
Tskiku Lonse
Tsiku Lonse
Wa m'mwamba m'mwamba
Wa M'mwamba m'mwamba
Ndidza mkweza tsiku
Lonse Lonse
Kwama siku onse
Wa M'mwamba m'mwamba
Ndidza mkweza tsiku
Lonse Lonse
Wa M'mwamba m'mwamba
Ndidza mkweza tsiku
Lonse Lonse
Kwama siku onse
Moyo wanga sangala Mulungu alinafe
Ona pepmphero lathu lija layankhidwadi
Nd'nakuuza padzana paja
Usa Kaikire Kaikire iwe
Mulungu wathu amayankha munthawi yake
Palibe pemphero lomwe limataika
Moyo wanga tiye
Timu Kakamire kamikire iwe
Muyenera kulandira ulemu wanu
Chifukwa palibe amene anga ime nanu.
Moyo wanga iwe
Siiwe Wamasiye wamasiye iwe
Nyengo taziona tonse zikusintha
Ayi Simaloto Zachitikadi
Moyo wanga mvera
Timukamire kakamire
Yeah yeah yeah
Yeah yeah yeah
Lonse
(Timu Kakamire)
Kwa masiku onse
(Timu Kakamiire)
Yeah yeah yeah
Yeah yeah yeah
Lonse
(Timukakamire) X3
Wa M'mwamba m'mwamba
Wa M'mwamba m'mwamba
Ndidza mkweza tsiku
Lonse Lonse
Kwama siku onse
Wa M'mwamba m'mwamba
Ndidza mkweza tsiku
Lonse Lonse
Wa M'mwamba m'mwamba
Ndidza mkweza tsiku
Lonse Lonse
Kwama siku onse
Ambuye
mwakufuna kwanu
Ndi Mawu anu
Munalenga chilengedwe chanu
Ambuye
Ndi mzimu wanu
Munauzizira mpweya wanu
M'nandilenga muchi fanizo chanu
Ambuye
Pautatu wanu
Atate mwana ndi mzimu wanu
Mutamandike
Ambuye
Mwa chikondi chanu
Mwandipatsa mpatso yanu
Ndikuyimbira dzina lanu
Yeah yeah yeah
Yeah yeah yeah
Lonse
(Ndiku imbira dzina lanu)
Kwa masiku onse
(Ndiku imbira dzina lanu)
Yeah yeah yeah
Yeah yeah yeah
Lonse
(Ndiku imbira dzina lanu) X3
Wa M'mwamba m'mwamba
Wa M'mwamba m'mwamba
Ndidza mkweza tsiku
Lonse Lonse
Kwama siku onse
Wa M'mwamba m'mwamba
Ndidza mkweza tsiku
Lonse Lonse
Wa M'mwamba m'mwamba
Ndidza mkweza tsiku
Lonse Lonse
Kwama siku onse
Yeah yeah yeah
Yeah yeah yeah
Lonse
Kwa masiku onse
Ndiku kakamilani
Sindiku Kaikirani
Ndikulambirani
Tsiku lonse
Ndikuyamikirani
Ndikugwadirani
Ndi ku kakamirani
Tsiku lonse
Yeah yeah yeah
Yeah yeah yeah
Lonse
Kwa masiku onse
Ndiku kakamilani
Sindiku Kaikirani
Ndikulambirani
Tsiku lonse
Ndikuyamikirani
Ndikugwadirani
Ndi ku kakamirani
Tsiku lonse
Wam'mwamba m'mwamba