![Umodzi Malawi ft. Lungu Vybz](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/11/13/489be4ecd931464ead703f8ac1087330H3000W3000_464_464.jpg)
Umodzi Malawi ft. Lungu Vybz Lyrics
- Genre:Reggae
- Year of Release:2023
Lyrics
Malawi the warm heart of Africa
Yeah Yeah
Malawi is the warm heart of Africa
Ndadza ndi masomphenya
Adziko la Malawi
Olimbana ndi loto langa
Angotaya Nthawi
Ndadza ngati mneneri
Ndatumidwa ndi nkhani
Ndilongosole nkhani
Tsono mvetserani
Shout
Malawi
Mtima wofunda
Wachilumba Cha Africa
Malawi
Mulungu wakukumbuka
Yankho lako lafika
Malawi
Nthawi yakwana
Yoti Nyali yako iwale
Malawi
Ali ndi khutu amve
Ali ndi diso awone
Yeah yeah yeah Malawi
Yeah yeah yeah
Yeah yeah yeah Malawi
Lungu vybz tell them now
There are reasons now we have to come together
Malawi needs the unity forever and ever
Be wise, always be clever
There are reasons now only few of us remember
Could be the memories that didn't last
Our ancestors gave us values in the past
That we have to trust
They made sure, peace and love is a must
Malawi
Mtima wofunda
Wachilumba Cha Africa
Malawi
Mulungu wakukumbuka
Yankho lako lafika
Malawi
Nthawi yakwana
Yoti Nyali yako iwale
Malawi
Ali ndi khutu amve
Ali ndi diso awone
Yeah yeah yeah Malawi
Yeah yeah yeah
Yeah yeah yeah Malawi
Umodzi
One love yeah
Umodzi
Ndiwo umati bweretsa pamodzi
Chikondi
Ndicho chimati pukuta misonzi
Umodzi
Ndiwo umati bweretsa pamodzi
Chikondi
Ndicho chimati pukuta misonzi
Umodzi
Ndiwo umati bweretsa pamodzi
Chikondi
Ndicho chimati pukuta misonzi
Umodzi
Ndiwo umati bweretsa pamodzi
Chikondi
Ndicho chimati pukuta misonzi
Ine ndi lawi
Tonse ndife a Malawi
Ine ndi lawi
Tonse ndife a Malawi
One Love to Malawi
We say
Malawi
Mtima wofunda
Wachilumba Cha Africa
Malawi
Mulungu wakukumbuka
Yankho lako lafika
Malawi
Nthawi yakwana
Yoti Nyali yako iwale
Malawi
Ali ndi khutu amve
Ali ndi diso awone
Yeah yeah yeah Malawi
Yeah yeah yeah
Yeah yeah yeah Malawi
To the warm of Africa
Malawi
The warm heart of Africa
Yeah yeah yeah
Malawi is the warm heart of Africa