
WAMVA KULIRA KWAKO Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2024
Lyrics
Wamva kulira kwako wamva pemphero lako
Nthawi ya yankho lako ladza
Wamva kulira kwako wamva pemphero lako
Nthawi ya yankho lako ladza
Wamva kulira kwako wamva pemphero lako
Nthawi ya yankho lako ladza
Wamva kulira kwako wamva pemphero lako
Nthawi ya yankho lako ladza
Mayi okwera phiri kupempherera nyengo zanu
Musataye mtima konse amvetsera
Bambo osala kudya kusalira moyo wanu
Musataye mtima konse amvetsera
Hannah analibe mwana zinamtengera kupemphera
Ndipo Yehovah anampatsa
Mayi musataye mtima imani pa Ambuye
Ali okhulupilika nthawi zonse
Wamva kulira kwako wamva pemphero lako
Nthawi ya yankho lako ladza
Wamva kulira kwako wamva pemphero lako
Nthawi ya yankho lako ladza
Kuli Mulungu oyankha pemphero
Yemwe adali alipo adzakhala
Mu nyengo zonse satileka
Nyengo zivute zisavute
Yehova amamvetsera ana ake
Mau ake akunena pemphani mudzapatsidwa
Yehova ndi okhulupilika satileka
Anachilitsa odwala adaukitsa okufa
Ndi Mulungu wa mphamvu wa dzisomo
Wamva kulira kwako wamva pemphero lako
Nthawi ya yankho lako ladza
Wamva kulira kwako wamva pemphero lako
Nthawi ya yankho lako ladza