
Job nkachiwanda Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2023
Lyrics
Ndapeza job m'bale wanga 10 faifi pamwezi
Maloto ako aja eya tigula benz
Maloto anga ako, maloto ako anga,
Makolo adyera Nyama yothira zi anyezi
Nde! Atilemba ntchito abrazi...
Tayiphula game a Naz
Struggle tiyikhalira, tilemera
Pamenepa tinenepa zonse kunthazi.
Eyaditu broskie.
Talemera chonchi.
Koma uziwa chani, ndigayire imodzi.
Zimakoma tikamagawana malipoti
Ukandimana akulanda ambuye poti
Job n'kachiwanda Job n'kachiwanda
Jo! Jo! job n'kachiwandaaaaaa
Job n'kachiwanda Job n'kachiwanda
Jo! Jo! job n'kachiwandaaaaaa
Overall zabwino, osazelengezera.
Overall nkwabwino, kuzichengetera
Job offer arrival, osamawuza fans
Salary ikafika nkuwagayirako hunz
Nsanje , Nthenda kugonjetsa Malawi
Iwe Sunga ntchito yako pambali
Smiles all over ukamawathoka good news
Hate yokhayokha ma devil anawa man u
Job n'kachiwanda Job n'kachiwanda
Jo! Jo! job nkachiwandaaa
Job n'kachiwanda Job n'kachiwanda
Jo! Jo! job nkachiwandaaa
Job n'kachiwandaaa
Job n'kachiwandaaa
Job n'kachiwandaaa
Job n'kachiwandaaa