
Malawi Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2022
Lyrics
265 you get that landlocked Malawi
Warm heart of that Africa, We burn flames Malawi
Chambo chathu Abale, Wamkulu gule timvale
Tithyole dansi wombani beni, tisangalale Malawi
labantwana sivalin'gape Khunjani wethu funathe
Mwawuka dona, tili makora Mwahuno drip tivale
Karonga mama phikani mpunga, dende Nyama ndivinyake
Chiwaya ndiine we're bestfriends ndi Chilembwe
5 Bar yanyuwani Ndi Bestfriend pa Chigege
Cultural heritage are historical sites
Pa Dedza Pomwepa apa tikhwekhwelere zimwemwe
Zi Chambo nkokhakuno, go outside there isnt
Ndirande nkokha Kuno go outside there isn't
Malawi nkokha kuno go outside there isn't