Limba Mtima Lyrics
- Genre:Gospel
- Year of Release:2023
Lyrics
Yahhooooh uuwahh yehh yehh
Yahhooooh yehh yehh yahh yeahh yah wooowoo ayayaya yehhh eehh yehh yeyeyeeh oohh ohhhhh
Limba mtima mbale wanga
Welenga mau a Yesu
Iye analonjeza sadzakusiya ukakhulupilika mpaka kale kale werenga ananena ndithu
Limba mtima mbale wanga
Welenga mau a Yesu
Iye analonjeza sadzakusiya ukakhulupilika mpaka kale kale werenga ananena ndithu
Ndikamayenda mziko lino
Mavuto amachuluka ah
Matenda uphawi masiye aaah
Zonsezi zindisowetsa chochitaa ahh
Koma ichi chokha ine ndidziwa mmhh
Ndili naye kalonga wamtendere-eh
Mphamvu yake njoposa yina yonse yihhii
Iye amasunga moyo wanga
Tsono limba mtima iwee--eeeh
Limba mtima mbale wanga
Welenga mau a Yesu
Analonjeza
Iye analonjeza sadzakusiya ukakhulupilika mpaka kale kale werenga ananena ndithu
Limba mtima limbatima we
Limba mtima mbale wanga
Iwe uwerenge mawu
Werenga mau a Yesu
Aaahh nalonjeza
Iye analonjeza sadzakusiya ukakhulupilika mpaka kale kale werenga ananena ndithu
Kumbukira m'bale nkhani yo yobu uyo
Ndi yosefe ogulitsidwa yooh
Omwe nthawi itawakwanila Yehhe-e-ehova anawadalitsaa
Ndipo ichi chokha m'bale udziwe iwe
Alipo kalonga wamtendere-eh
Tangosankha kutsamira pa iye hiiyih
Iye adzasunga moyo wako weee
Limba mtima mbale wanga
Iwe uwerenge mawu
Welenga mau a Yesu
Ohhh analonjeza
Iye analonjeza sazakusiya ukakhulupilika mpaka kale kale werenga ananena ndithu
Limba mtima limba mtima we
Limba mtima mbale wanga
Iwe uwerenge mawu wo
Welenga mau a yesu
Aaahh nalonjeza
Iye analonjeza sadzakusiya ukakhulupilika mpaka kale kale werenga ananena ndithu
Dziwaa
Mdima ungakule usiku-uuh
Mmawa umafikabe-ehh
Chilimwe chingakhale--eeh
Dzinja limafika ndithu--uuuh
Mavuto angachuluke-eeh
Ambuye adzathetsa ndithuu-uuh
Iwee--eeeh
Limba mtima mbale wanga
Iwe uwerenge mawu
Welenga mau a Yesu
Analonjeza
Iye analonjeza sadzakusiya ukakhulupilika mpaka kale kale werenga ananena ndithu
Limba mtima iweee
Limba mtima mbale wanga
Limba mtima iwe
Welenga mau a yesu
Werenga mauwo nalonjeza mbuye sadzakusiya
Iye analonjeza sadzakusiya ukakhulupilika mpaka kale kale werenga ananena ndithu
Limbamtima limba mtima
Limba mtima tima mbale wanga
Ulimbe mtima Yesu aliko
Welenga mau a Yesu
Adziwa mabvuto ako adzathetsa
Iye analonjeza sadzakusiya ukakhulupilika mpaka kale kale werenga ananena ndithu
Limba mtima limbatima
Limba mtima mbale wanga
Iweee uwerenge mawuu
Welenga mau a Yesu
Ambuye analonjeza sadzakusiya iwe oh
Iye analonjeza sadzakusiya ukakhulupilika mpaka kale kale werenga ananena ndithu