Mwa Chisomo Lyrics
- Genre:Gospel
- Year of Release:2023
Lyrics
Ndinachita zabwino
Kuthandiza ovutika
Ndinakhulupilika kumpingo
Kufunakuna chipulumutso
Ndinasunga malamulo
Kuchokera kuumwana wanga
Zonsenzo sizinathe
Kundigulira moyo osatha
Mwandipulumutsa mwachisomo ambuyeeee!!
Ndinasochera kutali koma mbuye mwandibweza mwandilunjikitsa kuufumu wanu wo
Ndikapeze moyo
Ndikapeze moyo inee ehhh
Ndikanali muutchimo
Ndikadali muutchimo mbuye munandifera mwachisomo chanu mwandipulumutsa ine
Osati kamba ka ntchito zabwino ndingachite
Ndinasochera kutalii ine!!!

(Ambuyeee mbuyee!!! )
Ndikadali muutchimo mbuye munandifera mwachisomo chanu mwandipulumutsa ine osati kamba ka ntchito zabwino ndingachite
Ntchito zanga zabwino pamaso panu mbuye zili ngat sanzaa
Ndipo sindiyenera konse
Ndimagwidwa ndimatha
Ndikachimwira dala
Mbuye mundiphuzitse ndiyere
Ndisaseweretse mwai wu
Poti Mwachisomo !!
Ndinasochera kutali koma mbuye mwandibweza mwandilunjikitsa kuufumu wanu wo
Ndikapeze moyo
Ndikapeze moyo inee ehhh
Ndikanali muutchimo
Ndikanali muutchimo mbuye munandifera mwachisomo chanu mwandipulumutsa ine
Osati kamba ka ntchito zabwino ndingachite
Ndinasochera kutalii ine!!!
Ndinasochera kutali koma mbuye mwandibweza mwandilunjikitsa kuufumu wanu wo
Ndikapeze moyo
Ndikapeze moyo inee ehhh
(Ambuyeee mbuyee!!! )
Ndikanali muutchimo
Ndikadali muutchimo mbuye munandifera mwachisomo chanu mwandipulumutsa ine osati kamba ka ntchito zabwino ndingachite
Lero ndamasuludwa
Ndilinayo mphamvu
Yofikira kumpando wanu
Komwe ndimapezako chifundo
Ndiimba ndichimwemwe poti ndapeza moyo
Koma sikutha kwanga ine
Kapena mphamvu zanga
Mwandipulumutsa mwachisomo!!