Alema Lyrics
- Genre:Afrobeats
- Year of Release:2023
Lyrics
Alema - K millian
...
namupeza ankala misozi mumanso mwe nivichani baby bwela uni uze, ati pali ve namvela pali mweo siniziba navo chita nalema navo nkansi muma enda kuti mukachokela kunchito simumabwela ku nyumba paka kwafipa bushe nimfuseko ndine mukazi wanu nangu wanchito ine noganiza