Babili Lyrics
- Genre:Afrobeats
- Year of Release:2023
Lyrics
Babili - K millian
...
K Millian
Kalandanya Music Promotion
Take over
This is a Jerry Fingers Production
Beauty lies in the eyes of the beholder aye
Ndiwe wanga ine
Personal decoder aye
Kutipatulula ise koma
Mulungu akamba
Ndiwe wanga ine
Mpaka imfa
Mkwati kunda te babili babili babili
Muchitemwiko te babili babili babili
Namumachuchi te babili babili
Ndiwe wanga babe mpaka imfa
Kuchokela pe tinapezana
Wenze kukuuza tizipiza kasewenza
Ati mina nakuthesa
Sungakonde mumthu monga ine yi
Ine eh
Manje nifuseko
Ndani abulika chikondi pa ziko lino eh
Ushe ni pastor nango kawalala
Nango nimumtu aliyense ali paziko la Mulungu
Beauty lies in the eyes of the beholder aye
Ndiwe wanga ine
Personal decoder aye
Kutipatulula ise koma
Mulungu akamba
Ndiwe wanga ine
Mpaka imfa
Mkwati kunda te babili babili babili
Muchitemwiko te babili babili babili
Namumachuchi te babili babili
Ndiwe wanga babe mpaka imfa
Ooh ati mona lomba
Nichitemwiko chakusani
Chigawale dauda