
Sindibwelera (Live recording) Lyrics
- Genre:Afrobeats
- Year of Release:2022
Lyrics
Ndisanabaswe, Munandidziwa
Ndisanalire, Mwapuputa misonzi yanga
Ndikasochera sochera mu'dima
Mundiunikira njira
Mchikondi chanu, Mtendere ndaupeza
Ndisanabaswe, Munandidziwa
Ndisanalire, Mwapuputa misonzi yanga
Ndikasochera sochera mu'dima
Mundiunikira njira
Mchikondi chanu, Mtendere ndaupeza
Ndaupeza
Sindibwelera m'buyo
Kapena kuyang'ana kumbali
Mpaka ndikafike
Kaya andinene
Sindibwelera m'buyo
Kapena kuyang'ana kumbali
Mpaka ndikafike
Kaya andiseke
Sindibwelera
Sindibwelera
Sindibwelera
Sindibwelera
Ndisanafooke,
Mwandipatsa nyonga
Ndipo phazi langa lisanatelereke
Mwandigwira dzanja
Ndikasochera sochera mu'dima
Mundiunikira njira
Mchikondi chanu, Mtendere ndaupeza
Ndaupeza
Sindibwelera m'buyo
Kapena kuyang'ana kumbali
Mpaka ndikafike
Kaya andinene
Sindibwelera m'buyo
Kapena kuyang'ana kumbali
Mpaka ndikafike
Kaya andiseke
Sindibwelera
Sindibwelera
Sindibwelera
Sindibwelera
Ayayo yoyo
Ayayo yoyo
Ayayo yoyo
Ayayo yoyo
Ayayo yoyo
Ayayo yoyo
Ayayo yoyo
Ayayo yoyo
Sindibwelera m'buyo
Kapena kuyang'ana kumbali
Mpaka ndikafike
Kaya andinene
Sindibwelera m'buyo
Kapena kuyang'ana kumbali
Mpaka ndikafike
Kaya andiseke
Sindibwelera
Sindibwelera
Sindibwelera
Sindibwelera