Alamu Anu (feat. Malaulo)
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2015
Lyrics
We hereee Poyamba kumupenya panali chapa geli anzake ankandiuza mkaziyu ndi sisiteli ukafuna kugwira amapereke theche ndi mistake kuyesa mwai mkaziyu sangatheke anayesa kunjanja ankayesa mabodza anayesa kudoja fans inandiyesa zoba koma 2 mina mina fanz pozazindikila celba ndi Sanudi mkaziuja wagwira ine ndi waku Nkhata iwe ngwaku Mangochi ine nkaponya kachitonga iwe udziponya ka Chiyao ine ndimkrisitu iwe ngwachisilamu ndikati go deeper iwe mkumati halaamu zosiyana zambiri ine ndalamu anu anthu angakambe zambiri za ine ndalamu anu timadziwa samadziwa zomwe timadziwa nde ndizakhalabe ine ndi alamu anu Usayese kundikokaaa,kundikanganuraaa upara mulanduu palibe chondiletsa kundilekanitsa ndi alamu anuuu usayese kundichotsaa,kundikanganuraaa upara mulanduu palibe chondiletsa kundilekanitsa ndi alamu anuu
Similar Songs
More from Macelba
Listen to Macelba Alamu Anu (feat. Malaulo) MP3 song. Alamu Anu (feat. Malaulo) song from album Alamu Anu (feat. Malaulo) is released in 2015. The duration of song is 00:03:30. The song is sung by Macelba.
Related Tags: Alamu Anu (feat. Malaulo), Alamu Anu (feat. Malaulo) song, Alamu Anu (feat. Malaulo) MP3 song, Alamu Anu (feat. Malaulo) MP3, download Alamu Anu (feat. Malaulo) song, Alamu Anu (feat. Malaulo) song, Alamu Anu (feat. Malaulo) Alamu Anu (feat. Malaulo) song, Alamu Anu (feat. Malaulo) song by Macelba, Alamu Anu (feat. Malaulo) song download, download Alamu Anu (feat. Malaulo) MP3 song
Comments (1)
New Comments(1)
linah8nlf7
love thi song