- Genre:Soul
- Year of Release:2021
Lyrics
Mtima wanga unasweka ndinkayesa nga wako ndiine ndekha
Zaka zitatu zongobetsa
Kundinamiza nnati ulipo wekha
Ndi Chikondi chakhathikhathi ndinakupatsa moyo wanga mosabwenza
Pano ntima uli madzi nsozi watsikila komwe unawubwenza
Kuti ukhale ntima mwanga
Sindingathe darli wanga
Wandipha mmoyo mwanga
Waupha ntima wanga
Kuti ukhale bwenzi langa
Sindingathe darli wanga
see lyrics >>Similar Songs
More from Teddy Makadi
Listen to Teddy Makadi Mtima MP3 song. Mtima song from album Mtima is released in 2021. The duration of song is 00:03:32. The song is sung by Teddy Makadi.
Related Tags: Mtima, Mtima song, Mtima MP3 song, Mtima MP3, download Mtima song, Mtima song, Mtima Mtima song, Mtima song by Teddy Makadi, Mtima song download, download Mtima MP3 song