
Mtima_Wanga
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2025
Lyrics
Life is unpredictable
Chonde mtima wanga uzidekha
Kumasamala popanga zisankho
Tsogolo lako si udindo wa anthu ena
Osamapusitsika ndi za pa social media
Kuseli kwa ma post ambiriwa akuvutika
Kumapempha nzeru zinthu zikakukulira
Size ilibe ntchito nyengo zikafuna kusintha
Zomwe umafuna pena si zomwe umazipeza
Koma osamazipatsa unnecessary pressure
see lyrics >>Similar Songs
More from Tact
Listen to Tact Mtima_Wanga MP3 song. Mtima_Wanga song from album Chomwe_Ndili_Extended Playlist is released in 2025. The duration of song is 00:03:06. The song is sung by Tact.
Related Tags: Mtima_Wanga, Mtima_Wanga song, Mtima_Wanga MP3 song, Mtima_Wanga MP3, download Mtima_Wanga song, Mtima_Wanga song, Chomwe_Ndili_Extended Playlist Mtima_Wanga song, Mtima_Wanga song by Tact, Mtima_Wanga song download, download Mtima_Wanga MP3 song