- Genre:Others
- Year of Release:2024
Lyrics
Mmmmmmh ooooooh ooooooh Akuzike Thawe yeahhhhhhhhh eeh eeh
Pomwepo Yesu anadza ndi iwo kumalo otchedwa Getsemani nanena kwa ophunzira ake Bakhalani inu pompano, ndipite uko ndikapemphere
Ndipo anatenga Petro ndi ana awiri a Zebedeo pamodzi naye nayamba kugwidwa ndi chisoni ndi kuthedwa nzeru
Ndipo anadza kwa ophunzira nawapeza iwo ali m'tulo nanena kwa Petro Nkutero kodi? Simungathe kuchezera ndi Ine mphindi imodzi?
Chezerani ndi kupemphera kuti mungalowe m'kuyesedwa: mzimutu uli wakufuna koma thupi lili lolefuka
Pamenepo ananena kwa iwo Moyo wanga uli wozingidwa ndi chisoni cha kufika nacho kuimfa; khalani pano muchezere pamodzi ndi Ine Ndipo anamuka patsogolo pang'ono nagwa nkhope yake pansi napemphera nati Atate ngati nkutheka chikho ichi chindipitirire Ine koma si monga ndifuna Ine koma Inu
Ndipo anadza kwa ophunzira nawapeza iwo ali m'tulo nanena kwa Petro Nkutero kodi? Simungathe kuchezera ndi Ine mphindi imodzi?
see lyrics >>Similar Songs
More from Akuzike Thawe
Listen to Akuzike Thawe Getseman MP3 song. Getseman song from album Acts Of The Apostle is released in 2024. The duration of song is 00:03:37. The song is sung by Akuzike Thawe.
Related Tags: Getseman, Getseman song, Getseman MP3 song, Getseman MP3, download Getseman song, Getseman song, Acts Of The Apostle Getseman song, Getseman song by Akuzike Thawe, Getseman song download, download Getseman MP3 song