
Ungondibwelenzera
- Genre:World Music/Folklore
- Year of Release:2023
Lyrics
Ungondibwelenzera - Lulu & Mathumela Band
...
Nkhope Yako yasintha
siyomwe ija ndimadziwa,
siyomwe unkandiwonetsa pondifuna,
malankhulidwe asintha, wayamba kukweza mawu simomwe unkandilankhulira pondifuna, unkakamba mawu a nzeru Kumandilonjeza za zambiri munalipo ambiri koma iwe kundiwina
unkakamba za nzeru mawu Ako olimbikitsa papita nthawi ndifuna ndimveso kawiri
chorus
honey honey ooo
sinfuna chinthu china
ungondibwerezera(zimene unkandiuza ndisanakulore)
honey musachotsere mawu kapena kuonjeza
see lyrics >>Similar Songs
More from Lulu & Mathumela Band
Listen to Lulu & Mathumela Band Ungondibwelenzera MP3 song. Ungondibwelenzera song from album Mwayenera is released in 2023. The duration of song is 00:04:59. The song is sung by Lulu & Mathumela Band.
Related Tags: Ungondibwelenzera, Ungondibwelenzera song, Ungondibwelenzera MP3 song, Ungondibwelenzera MP3, download Ungondibwelenzera song, Ungondibwelenzera song, Mwayenera Ungondibwelenzera song, Ungondibwelenzera song by Lulu & Mathumela Band, Ungondibwelenzera song download, download Ungondibwelenzera MP3 song