Ulemelero Wanu ft. Praise Umali Lyrics
- Genre:Gospel
- Year of Release:2022
Lyrics
Ulemelero Wanu ft. Praise Umali - Free Worship Malawi
...
ulemelero wanu ukhale nthawi zonse
ambuye kondwerani ndi ntchito yamanja anu
ulemelero wanu ukhale nthawi zonse
Ambuye kondwerani ndi ntchito yamanja anu
Ine ndidzakuyimbirani ndikadali ndi moyo ndidzalemekeza Inu ndi umuthu wanga onse
ine ndidzakuyimbirani ndikadali ndi moyo ndidzalemekeza Inu ndi umuthu wanga onse
ulemelero wanu ukhale nthawi zonse ambuye kondwerani ndi ntchito yamanja anu
ulemelero wanu ukhale nthawi zonse ambuye kondwerani ndi ntchito