Sunga ft. Leslie & Bobby Cling Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2022
Lyrics
Wamusowa usakane
Kumuwona ndi wina zimawawa
Yeah (Sungamuiwale)
Zimandibowa, mkamukuona ndi iyeyo
Mmhu... Okukonda ndi ineyo
Just know that you will always be my baby, sindingaiwale no!
Umadabwa nchani chinachitika
Ndinalakwisa chani kuti azinditsika
Ndinkangomva zoti mwamuna amalira
Ndazionera ndekha ndipo ndine osweka mtima
Simngaiwale zonse zonwe tinkapanga
Ma plan tinkapanga, chidale changa utachisamila
Mtendere wa mu mtima sunali nkhani zanga zinali wello, osadziwa zizasintha
Sungamuiwale amene unkakondwa naye
Sungafufute nyengo zonse munadusamo
Sungamuiwale, sungamuiwale
Sungamuiwale, sungamuiwale
Sungamuiwale amene unkakondwa naye
Zimandibowa, mkamukuona ndi iyeyo
Mmhu.. Okukonda ndi ineyo
Just know that you will always be my baby, sindingaiwale no! uhmm
Bvuto (Bvuto) ine singamuiwale
Maine maine, no matter how many times you try
Mbuye anakudalitsa ndi mtima wa chikondi
Mwa iwe ndaphunziramo chikondi
Tinali noninoni, kuyenda pansewu mnali ndi khonfi
Pano ndimangozimvera chisoni
Za - khaladi chonchi, ndithudi masiku sakoma onse
Masaya angozaza ndi misozi
Really I get lonely, usiku osagona, mtendere osaupeza
Sindinkadziwa zizakhala chonchi
Simngaiwale, mtima wanga udakonda iwe darling
Awa angonditayisa nthawi chabe
Mtima wanga udasankha iwe mamiiiie... eh
Sungamuiwale amene unkakondwa naye
Sungafufute nyengo zonse munadusamo
Sungamuiwale, sungamuiwale
Sungamuiwale, sungamuiwale
Sungamuiwale amene unkakondwa naye
Pano nthawi yadusa ndakusowa simngakane eh
Kukuwona ndi wina zimawawa simngakane
Eh!
Ndithu ndimakupangila nsanje
Mu mtima mwanga zimawawabe
Mnalakwisa cha kuti undithawe
Ndimakusowa daily iwe darling
Oh! Oh! Oh! Ndimakusowa, ndimakusowa
Oh! Oh! Oh! Palibe wina, palibe wina