![Mose](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/11/11/a4c7c6b5a98c42fbbeb7a3ea9df182dd_464_464.jpg)
Mose Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2021
Lyrics
Ndili Paulendo wa Mose
Sindinga Gonje
Palibe Ku Topa
Palibe Ku wopa
Kuwoloka nyanja yo fila
Madzi kundi patukila
Poyenda ndi da lalikila
Sindi Ku wopa Ku Mila
Nda gwila ndodo ya Mose
Sindinga Gonje
Palibe Ku Topa
Palibe Ku wopa
Kuwoloka nyanja yo fila
Madzi kundi patukila
Poyenda ndi da lalikila
Sindi Ku wopa Ku Mila
Ndida chiwona chimoto
Chikungo yaka muntengo
Chi da ndi patsa uthenga
Umvetsele Namalenga -
Ada ndi patsa chi mtengo
Ada ndi patsa uthenga
Ada ndi patsa lonjezo
Kumeneko muchokeko-
Nthawi yomweyo pemphelo
Kudango dutsa chi mphepo
Then I started seeing visions
I was apart of the mission
Kukumana ndi Adani
Tonse Ku sowa ma plani
Ambuye Ada gwetsa madzi
Satana Ku Chita Manyazi
Ndili Paulendo wa Mose
Sindinga Gonje
Palibe Ku Topa
Palibe Ku wopa
Kuwoloka nyanja yo fila
Madzi kundi patukila
Poyenda ndi da lalikila
Sindi Ku wopa Ku Mila
Nda gwila ndodo ya Mose
Sindinga Gonje
Palibe Ku Topa
Palibe Ku wopa
Kuwoloka nyanja yo fila
Madzi kundi patukila
Poyenda ndi da lalikila
Sindi Ku wopa Ku Mila