Ma Luv Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2021
Lyrics
Ma Luv - Martse
...
Martse
Yeah yeah yeah yeah
zama love ndikukuwuzani you can die iwe
tiyeni tizingomwa mowawu ma guy yeah yeah
zama love ndikukuwuzani you can die tiyeni tizingomwa mowawu ma guy
awo aku votter sakudwala ndikukuwuzani zama love you can die
kukanika kuphaka appetite sikubwela zama love you can die
Tulo silikubwela chavuta nchani anthuni
mtima mwanga muli nkhondo muli zibauti
koma zomwe akupanga alamu anuzi
kundiyika under pressure pano pa town
I think apeza njonda
mwano okhaokha ati chibwez ichichi mwasalamo nokha
akut atopa akufuna kuchoka
akut tayamba kusiyana ngini zokonda
anavaya ku party ndi achina Jen
akumana ndima yooh oziwa make a train
kubwela kwa ineyo kumazandimvesa pain
kenako amvekele kuti it's just a phase
zama love ndikukuwuzani you can die iwe
tiyeni tizingomwa mowawu ma guy ×2
awo aku votter sakudwala ndikukuwuzani zama love you can die iwe kukanika kuphaka appetite sikubwela zama love you can die iwe
Halima adandaula za Daud, amakambilanaso ndi Sharon akuti kukhalangati wapeza mami mu town
shart ija yabwela make up wa brown
akumanjanjanjanja olo kundihaga
ati msima ndisaphika akadya wakawaka
phone ijaso waika ma password aja
kwasalaku mumva kuti banja latha
anapita ku party ndima boys
ndiye umaziwa akakhala ndi achina Loud
nkhani ya akazi imakhala chi topic
kwathu ndilinako ndithu I'm going
zama love ndikukuwuzani you can die iwe
tiyeni tizingomwa mowawu ma guy yeah yeah
zama love ndikukuwuzani you can die iwe tiyeni tizingomwa mowawu ma guy
awo aku votter sakudwala ndikukuwuzani zama love you can die
kukanika kuphaka appetite sikubwela zama love you can die iwe
kundidyesa flas ndizingogwila bottle ndithu kuipasa moto
zondiswela mtima ndati ine toto ndithu kuipasa moto×2
zama love ndikukuwuzani you can die iwe tiyeni tizingomwa mowawu ma guy yeah yeah×2
awo aku votter sakudwala ndikukuwuzani zama love you can die iwe
kukanika kuphaka appetite sikubwela zama love you can die iwe
iwe