
I'M READY ft. Zocorah Ike Mw Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2025
Lyrics
Bbe O bbe
Honey O honey
I'm ready to spend my life with you
I like the way you call me honey honey
I like the way you call me Sweetie sweetie
I like the way you call me honey honey
I like the way you call me Sweetie sweetie
E ndimakukonda honey ndimakukondaa
Sindizakusiya honey sindizakusiyaa
Chikondi chathu Bbe chikondi chathu
Mpakana infa mpakana mmanda
Sono bwela tivine tijaive tinyadire
Poti zoteledzi zimasowa Bbe wee
Sono bwela tivine tijaive tinyadire
Poti zoteledzi zimasowa honey wee
Bbe O bbe
Honey O honey
I'm ready to spend my life with you
Makolo anga ndinawaudza kale za iwe
Kuti chaka chino ndikumanga oyela
Kwa ma hope onse ndinakhwantchisa kale Bbe
Kuti nthiti yanga Sono ndaipedza
Ndatopa kusitha sitha
Nthiti yanga ndaipedza
Ndikufuna kukhadzikika mwa iweyo for ever
Ndatopa kusitha sitha
Nthiti yanga ndaipedza
Ndikufuna kukhadzikika mwa iweyo for ever