![Kwathu](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/01/28/27b2325b5f18406b8a740360d74b5c65H3000W3000_464_464.jpg)
Kwathu Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2023
Lyrics
Ama hater tikatsogola.
Ife nde tikucontroller.
tidakalibe kukolola.
Ife kwathu ndi ku mpanje.
Sindingapange nawe tu manjenje.
Uka ndi koka ugwera mu dzenje.
Man ah man sangakhale mbembembe
I've been trying to stay out of the mix.
You don't really know how ot feels.
I've been trying to stay out of the mix.
You don't really know how it feeeeels.
Kwathu ndi ku Mpanje.
Anthu amayankhula.
Kwathu ndi ku mpanje tizayiphulaaaa.
Kwathu ndi ku mpanje.
Kwathu ndi ku mpanje.
Kwathu ndi ku Mpanje.
Kwathu ndi ku Mpanje eeh.
I've been trying to stay out of the mix You don't really know how it feels.
I've been trying to stay out of the mix. you don't really know how it feels.
Ife kwathu ndi ku malawi.
Petrol timagula mu 5 litre.
Ukhale broke nkazi sachedwa kutsika.
Ndipange bwanji ndingomenya aviator.
Early in the morning get the bag.
Kusaka vepi boi you can't relax.
I aint stopping till i get the cash.
If i Catch an a L i'll make it baaack.
I've been trying to stay out of the mix.
You don't really know how ot feels.
I've been trying to stay out of the mix.
You don't really know how it feeeeels.
Kwathu ndi ku Mpanje
Anthu amayankhula.
Kwathu ndi ku mpanje
Tizayiphulaaaa.
Kwathu ndi ku mpanje.
Kwathu ndi ku mpanje.
Kwathu ndi ku Mpanje.
Kwathu ndi ku Mpanje eeh.