Waimanya Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2024
Lyrics
Waimanya - JETU MW
...
Iwe ndi ndani ine ndi Jetu
Muli nd pakamwa
eya palibe kukulesani kuyankhula
koma muphunzire kujama yanu
one day muzakhawula
Kodi tachezesa nenani
akuvuta macheza nenani
akudana ndi Jetu
tisiye kucheza ingonenani
kodi tachezesa nenani
akuvuta macheza nenani
akudana ndi Jetu
tisiye kucheza ingonenani
koma zoti ndine dolo wayimanya
anandituluka wayimanya
walemba mmadzi wayimanya
wayi wayi ee wayimanya
koma zoti ndine dolo wayimanya
anandituluka wayimanya
walemba mmadzi wayimanya
wayi wayi wayimanya
Mdalitso wanga sungakhale wanu
azimnzanga sangakhale wanu
muphunzire kumajama yanu
ngati zikuvuta ndikupaseni ganyu
atangotola chikwama
anasintha kukhala olongolora
ndiye
u better mind your business
usanditipese
bwanji mundisiye
ndili ndi zonena Kwa nonse ma haters
zilekeke zomalondana ma pazi
ulilane nza bwino osat jealous
koma zikuvuta tizakokana ma shirt