
Zikomo Lyrics
- Genre:Gospel
- Year of Release:2024
Lyrics
Ambuye ndabwela, mbuye ndabwela
Kuyamikila chisomo chanu
Ambuye ndabwela, mbuye ndabwela
Kuyamikila chikondi chanu
Zikomo, zikomo, zikomo, zikomo
Zikomo, zikomo ambuye eeeeeh
Ndinali ndani popanda inu
Ndinali ndani ine eeeh popanda inu
Mwandisambitsa, mwandiyeretsa
Mwandikwezeka, mwanditukula oooh
Zikomo, zikomo, zikomo, zikomo
Zikomo, zikomo ambuye eeeeeh
Munandidziwa ndisanababwe
Mundandiona ndili mmatope
Munandifera ndili ochimwa
Chikondi chanji
Chikondi chanji chopanda tsankho
Chikondi chanji chopanda malile
Zikomo, zikomo, zikomo, zikomo
Zikomo, zikomo ambuye eeeeeh