Like So Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2024
Lyrics
You should've waited
Munafela Mercedes
Mkazi wozala ndi M'dede
Tsk aaahh
Munakadekha Kaye Mamie
Sumadziwa I had plans for you
Make you mine have a kid or 2
With a wedding so colorful oooh
Azimayi nthungululu
Nde pano ndili better
Ndaphuzila ku betcha
Ndi ine chi mfana chobeba
Sindimakukondaso
So
Wandikonda bwanji lero?
(Unandikana ndili zoba ineyo)
Ukufuna ndikuveke velo
(Pano chifukwa zinthu zanga zili bhou)
Sindimakukondaso
So
So
Ooo I don't love you like so
So
So
Ooo
Undikonda bwanji lero?
(Unandikana ndili zoba ineyo)
Ukufuna ndikuveke velo
(Lero chifukwa zinthu zanga zili wello)
Sindimakukondaso
So
So
Ooo I don't love you like so
So
So
Ooo
Mesa unkati ndi ine Mphawi?
I can't afford you Mamie
Umafuna ma big boys with them big cars
Ndi phone ya apples woluma
Nde pano ndi ine big boy
Ndimathamangisa Mission
Ndalama zanga siza season
Nde sindingakusekelele
Kubwera ndi kamwa lokuthwa
Ukufuna undidyele eh eh
Sunandikonde at my worst
Nde usandikonde at my best
Poti pano ndili better
Ndaphuzila ku betcha
Ndi ine mfana obeba
Sindimakukondaso ooh
Wandikonda bwanji lero?
(Unandikana ndili zoba ineyo)
Ukufuna ndikuveke velo
(Pano chifukwa zinthu zanga zili bhou)
Sindimakukondaso
So
So
Ooo I don't love you like so
So
So
Ooo
Udikonda bwanji lero?
(Unandikana ndili zoba ineyo)
Ukufuna ndikuveke velo
(Lero chifukwa zinthu zanga zili wello)
Sindimakukondaso
So
So
Ooo I don't love you like so
So
So
Ooo