Muyende nane (Live) Lyrics
- Genre:Gospel
- Year of Release:2024
Lyrics
M’mene moyo wanga usowa chitonthozo
Mtima wanga ukafoka nasowa mphamvu
Ndiyangana kwa inu
Ndiyangana kwa inu
M’chigwa cha mthunzi wa imfa
Msandisiye ndekha
Ndidzipeleka kwa inu
Muchite nane
Tengani moyo wanga
Ukhale wanu
Tengani mtima wanga
Ukhale wanu
Ndilibe mphamvu zoyenda ndekha
Muyende nane
Ndilibe mphamvu zodzilimbitsa
Muyende nane
Muyende nane
Muyende nane
M’chigwa cha mthunzi wa imfa
Msandisiye ndekha
Ndidzipeleka kwa inu
Muchite nane
Tengani moyo wanga
Ukhale wanu
Tengani mtima wanga
Ukhale wanu
Ndilibe mphamvu zoyenda ndekha
Muyende nane
Ndilibe mphamvu zodzilimbitsa
Muyende nane
Muyende nane
Muyende nane
Mukhale nane
Mukhale nane
Muyime nane
Muyime nane